127
Q.S Al-A'raf (7:127)
وَقَالَ الْمَلَاُ مِنْ قَوْمِ فِرْعَوْنَ اَتَذَرُ مُوْسٰى وَقَوْمَهٗ لِيُفْسِدُوْا فِى الْاَرْضِ وَيَذَرَكَ وَاٰلِهَتَكَۗ قَالَ سَنُقَتِّلُ اَبْنَاۤءَهُمْ وَنَسْتَحْيٖ نِسَاۤءَهُمْۚ وَاِنَّا فَوْقَهُمْ قٰهِرُوْنَ
wa qālal-mala'u min qaumi fir‘auna atażaru mūsā wa qaumahū liyufsidū fil-arḍi wa yażaraka wa ālihatak(a), qāla sanuqattilu abnā'ahum wa nastaḥyī nisā'ahum, wa innā fauqahum qāhirūn(a).
Ndipo atsogoleri a anthu a Farao anati, “Kodi mulola Mose ndi anthu ake kuwononga dziko lino (Igupto) ndikusiya inu ndi milungu yanu?” (Farao) anayankha kuti, “Tidzapha ana awo aamuna ndi kulola ana awo aakazi kukhala ndi moyo ndipo ndithudi tili ndi mphamvu zonse pa iwo.”