116

Q.S Al-A'raf (7:116)

قَالَ اَلْقُوْاۚ فَلَمَّآ اَلْقَوْا سَحَرُوْٓا اَعْيُنَ النَّاسِ وَاسْتَرْهَبُوْهُمْ وَجَاۤءُوْ بِسِحْرٍ عَظِيْمٍ

qāla alqū, falammā alqau saḥarū a‘yunan-nāsi wastarhabūhum wa jā'ū bisiḥrin ‘aẓīm(in).

Iye (Mose) anayankha kuti, “Iponyeni (yoyamba)!” Choncho ataponya, analodza maso a anthu ndi kuwachititsa mantha, chifukwa anasonyeza matsenga akuluakulu (odabwitsa).