3
Q.S At-Taghabun (64:3)
خَلَقَ السَّمٰوٰتِ وَالْاَرْضَ بِالْحَقِّ وَصَوَّرَكُمْ فَاَحْسَنَ صُوَرَكُمْۚ وَاِلَيْهِ الْمَصِيْرُ
khalaqas-samāwāti wal-arḍa bil-ḥaqqi wa ṣawwarakum fa'aḥsana ṣuwarakum, wa ilaihil-maṣīr(u).
Iye adalenga kumwamba ndi dziko lapansi ndi cholinga choyenera, adapanga mawonekedwe anu kenako adakonza mawonekedwe anu, ndipo kwa Iye ndiko kubwerera.