12
Q.S At-Taghabun (64:12)
وَاَطِيْعُوا اللّٰهَ وَاَطِيْعُوا الرَّسُوْلَۚ فَاِنْ تَوَلَّيْتُمْ فَاِنَّمَا عَلٰى رَسُوْلِنَا الْبَلٰغُ الْمُبِيْنُ
wa aṭī‘ullāha wa aṭī‘ur-rasūl(a), fa'in tawallaitum fa innamā ‘alā rasūlinal-balāgul-mubīn(u).
Ndipo mverani Mulungu ndipo mverani Mtumiki. Ngati mutembenuka, ndiye kuti udindo wa Mtumiki wathu ndi kungonena momveka bwino (lamulo la Mulungu).