10

Q.S At-Taghabun (64:10)

وَالَّذِيْنَ كَفَرُوْا وَكَذَّبُوْا بِاٰيٰتِنَآ اُولٰۤىِٕكَ اَصْحٰبُ النَّارِ خٰلِدِيْنَ فِيْهَاۗ وَبِئْسَ الْمَصِيْرُ ࣖ

wal-lażīna kafarū wa każżabū bi'āyātinā ulā'ika aṣḥābun-nāri khālidīna fīhā, wa bi'sal-maṣīr(u).

Ndipo amene sakhulupirira ndi kukana zizindikiro zathu, amenewo ndi anthu okhala ku gehena, adzakhala komweko kwamuyaya. Ndipo kumeneko ndi malo oipa kwambiri obwererako.