88

Q.S An-Nisa (4:88)

۞ فَمَا لَكُمْ فِى الْمُنٰفِقِيْنَ فِئَتَيْنِ وَاللّٰهُ اَرْكَسَهُمْ بِمَا كَسَبُوْا ۗ اَتُرِيْدُوْنَ اَنْ تَهْدُوْا مَنْ اَضَلَّ اللّٰهُ ۗوَمَنْ يُّضْلِلِ اللّٰهُ فَلَنْ تَجِدَ لَهٗ سَبِيْلًا

famā lakum fil-munāfiqīna fi'ataini wallāhu arkasahum bimā kasabū, aturīdūna an tahdū man aḍallallāh(u), wa may yuḍlilillāhu falan tajida lahū sabīlā(n).

Nanga bwanji mukugawikana m'magulu awiri (motsutsana) ndi achinyengo, ngakhale kuti Mulungu wawabwezera (ku kusakhulupirira), chifukwa cha khama lawo? Kodi mukufuna kuwatsogolera anthu omwe Mulungu wawalola kusochera? Amene Mulungu walola kusochera, simudzapeza njira (yomutsogolera).