86

Q.S An-Nisa (4:86)

وَاِذَا حُيِّيْتُمْ بِتَحِيَّةٍ فَحَيُّوْا بِاَحْسَنَ مِنْهَآ اَوْ رُدُّوْهَا ۗ اِنَّ اللّٰهَ كَانَ عَلٰى كُلِّ شَيْءٍ حَسِيْبًا

wa iżā ḥuyyītum bitaḥiyyatin fa ḥayyū bi'aḥsana minhā au ruddūhā, innallāha kāna ‘alā kulli syai'in ḥasībā(n).

Ndipo ngati mwalemekezedwa ndi ulemu (wa moni), bwezerani ulemuwo ndi wabwino, kapena bwezerani (ulemu, womwe uli wofanana) nawo. Ndithudi, Mulungu amaganizira chilichonse.