64
Q.S An-Nisa (4:64)
وَمَآ اَرْسَلْنَا مِنْ رَّسُوْلٍ اِلَّا لِيُطَاعَ بِاِذْنِ اللّٰهِ ۗوَلَوْ اَنَّهُمْ اِذْ ظَّلَمُوْٓا اَنْفُسَهُمْ جَاۤءُوْكَ فَاسْتَغْفَرُوا اللّٰهَ وَاسْتَغْفَرَ لَهُمُ الرَّسُوْلُ لَوَجَدُوا اللّٰهَ تَوَّابًا رَّحِيْمًا
wa mā arsalnā mir rasūlin illā liyuṭā‘a bi'iżnillāh(i), wa lau annahum iẓ ẓalamū anfusahum jā'ūka fastagfarullāha wastagfara lahumur-rasūlu lawajadullāha tawwābar raḥīmā(n).
Ndipo sitinatumize Mtumiki koma kuti amveredwe ndi chilolezo cha Mulungu. Ndipo ndithudi, ngati atadzichitira okha zoipa, akabwera kwa iwe (Muhammad), napempha chikhululukiro kwa Mulungu, ndipo Mtumiki nayenso akawapempherera chikhululukiro, adzamupeza Mulungu Wolandira kulapa Kwambiri, Wachifundo Chambiri.