55

Q.S An-Nisa (4:55)

فَمِنْهُمْ مَّنْ اٰمَنَ بِهٖ وَمِنْهُمْ مَّنْ صَدَّ عَنْهُ ۗ وَكَفٰى بِجَهَنَّمَ سَعِيْرًا

fa minhum man āmana bihī wa minhum man ṣadda ‘anh(u), wa kafā bijahannama sa‘īrā(n).

Choncho pakati pa (anthu amene ali ndi nsanje), pali amene amamukhulupirira ndipo palinso amene amaletsa (anthu kuti asamukhulupirire). Jahena yomwe malawi ake amayaka imakwanira (kwa iwo).