50
Q.S An-Nisa (4:50)
اُنْظُرْ كَيْفَ يَفْتَرُوْنَ عَلَى اللّٰهِ الْكَذِبَۗ وَكَفٰى بِهٖٓ اِثْمًا مُّبِيْنًا ࣖ
unẓur kaifa yaftarūna ‘alallāhil-każib(a), wa kafā bihī iṡmam mubīnā(n).
Taonani momwe akupangira Mulungu mabodza! Ndipo kuchita zimenezo n’kokwanira kuti chikhale tchimo lenileni (kwa iwo).