Q.S An-Nisa (4:47)
يٰٓاَيُّهَا الَّذِيْنَ اُوْتُوا الْكِتٰبَ اٰمِنُوْا بِمَا نَزَّلْنَا مُصَدِّقًا لِّمَا مَعَكُمْ مِّنْ قَبْلِ اَنْ نَّطْمِسَ وُجُوْهًا فَنَرُدَّهَا عَلٰٓى اَدْبَارِهَآ اَوْ نَلْعَنَهُمْ كَمَا لَعَنَّآ اَصْحٰبَ السَّبْتِ ۗ وَكَانَ اَمْرُ اللّٰهِ مَفْعُوْلًا
yā ayyuhal-lażīna ūtul-kitāba āminū bimā nazzalnā muṣaddiqal limā ma‘akum min qabli an naṭmisa wujūhan fa naruddahā ‘alā adbārihā au nal‘anahum kamā la‘annā aṣḥābas-sabt(i), wa kāna amrullāhi maf‘ūlā(n).
E inu anthu amene mwapatsidwa Buku! Khulupirirani zimene tavumbulutsa (Qur'an) zomwe zikutsimikizira Buku lomwe lili nanu, tisanasinthe nkhope (zanu), kenako Tidzawabwezera m'mbuyo kapena Tidzawatemberera monga momwe Tidzatemberera anthu (ochita chiwerewere) pa Sabata (Loweruka). Ndipo lamulo la Mulungu lidzagwira ntchito ndithu.