45

Q.S An-Nisa (4:45)

وَاللّٰهُ اَعْلَمُ بِاَعْدَاۤىِٕكُمْ ۗوَكَفٰى بِاللّٰهِ وَلِيًّا ۙوَّكَفٰى بِاللّٰهِ نَصِيْرًا

wallāhu a‘lamu bi'a‘dā'ikum, wa kafā billāhi waliyyaw wa kafā billāhi naṣīrā(n).

Ndipo Mulungu amadziwa bwino za adani anu. Mulungu ndi wokwanira kukhala mtetezi ndipo Mulungu ndi wokwanira kukhala mthandizi (kwa inu).