30
Q.S An-Nisa (4:30)
وَمَنْ يَّفْعَلْ ذٰلِكَ عُدْوَانًا وَّظُلْمًا فَسَوْفَ نُصْلِيْهِ نَارًا ۗوَكَانَ ذٰلِكَ عَلَى اللّٰهِ يَسِيْرًا
wa may yaf‘al żālika ‘udwānaw wa ẓulman fa saufa nuṣlīhi nārā(n), wa kāna żālika ‘alallāhi yasīrā(n).
Ndipo amene achita izi mophwanya lamulo ndi mopanda chilungamo, tidzamuika ku gehena. Zimenezo n’zosavuta kwa Allah.