174
Q.S An-Nisa (4:174)
يٰٓاَيُّهَا النَّاسُ قَدْ جَاۤءَكُمْ بُرْهَانٌ مِّنْ رَّبِّكُمْ وَاَنْزَلْنَآ اِلَيْكُمْ نُوْرًا مُّبِيْنًا
yā ayyuhan-nāsu qad jā'akum burhānum mir rabbikum wa anzalnā ilaikum nūram mubīnā(n).
E inu anthu! Ndithudi, umboni wa choonadi wochokera kwa Mbuye wanu, (Muhammad ndi zozizwitsa zake) wafika kwa inu ndipo takutumizirani kuunika kowala (Qur'an).