170
Q.S An-Nisa (4:170)
يٰٓاَيُّهَا النَّاسُ قَدْ جَاۤءَكُمُ الرَّسُوْلُ بِالْحَقِّ مِنْ رَّبِّكُمْ فَاٰمِنُوْا خَيْرًا لَّكُمْ ۗوَاِنْ تَكْفُرُوْا فَاِنَّ لِلّٰهِ مَا فِى السَّمٰوٰتِ وَالْاَرْضِۗ وَكَانَ اللّٰهُ عَلِيْمًا حَكِيْمًا
yā ayyuhan-nāsu qad jā'akumur-rasūlu bil-ḥaqqi mir rabbikum fa āminū khairal lakum, wa in takfurū fa inna lillāhi mā fis-samāwāti wal-arḍ(i), wa kānallāhu ‘alīman ḥakīmā(n).
E inu anthu! Ndithudi, Mtumiki (Muhammad) wabwera kwa inu ndi choonadi chochokera kwa Mbuye wanu, choncho khulupirirani (mwa iye), ndibwino kwa inu. Ndipo ngati simukhulupirira (sichidzavulaza Mulungu ngakhale pang'ono) chifukwa Mulungu ndi wa zonse zakumwamba ndi zapadziko lapansi. Mulungu ndi Wodziwa Zonse, Wanzeru Zonse.