17

Q.S An-Nisa (4:17)

اِنَّمَا التَّوْبَةُ عَلَى اللّٰهِ لِلَّذِيْنَ يَعْمَلُوْنَ السُّوْۤءَ بِجَهَالَةٍ ثُمَّ يَتُوْبُوْنَ مِنْ قَرِيْبٍ فَاُولٰۤىِٕكَ يَتُوْبُ اللّٰهُ عَلَيْهِمْ ۗ وَكَانَ اللّٰهُ عَلِيْمًا حَكِيْمًا

innamat-taubatu ‘alallāhi lil-lażīna ya‘malūnas-sū'a bijahālatin ṡumma yatūbūna min qarībin fa ulā'ika yatūbullāhu ‘alaihim, wa kānallāhu ‘alīman ḥakīmā(n).

Ndithudi, kulapa kwa Mulungu ndi kwa anthu okhawo amene amachita zoipa chifukwa cha kusadziwa, kenako n’kulapa nthawi yomweyo. Kulapa kwawo ndiko komwe Mulungu amavomereza. Mulungu ndi Wodziwa Zonse, Wanzeru Zonse.