161

Q.S An-Nisa (4:161)

وَّاَخْذِهِمُ الرِّبٰوا وَقَدْ نُهُوْا عَنْهُ وَاَكْلِهِمْ اَمْوَالَ النَّاسِ بِالْبَاطِلِ ۗوَاَعْتَدْنَا لِلْكٰفِرِيْنَ مِنْهُمْ عَذَابًا اَلِيْمًا

wa akhżihimur-ribā wa qad nuhū ‘anhu wa aklihim amwālan-nāsi bil-bāṭil(i), wa a‘tadnā lil-kāfirīna minhum ‘ażāban alīmā(n).

Ndipo chifukwa chakuti amachita katapira, ngakhale kuti aletsedwa kutero, ndi chifukwa chakuti amadya chuma cha anthu mopanda lamulo (batil). Ndipo tawakonzera chilango chowawa kwa osakhulupirira pakati pawo.