156
Q.S An-Nisa (4:156)
وَّبِكُفْرِهِمْ وَقَوْلِهِمْ عَلٰى مَرْيَمَ بُهْتَانًا عَظِيْمًاۙ
wa bikufrihim wa qaulihim ‘alā maryama buhtānan ‘aẓīmā(n).
ndipo (Tidawalanganso) chifukwa cha kusakhulupirira kwawo (Yesu), ndi milandu yawo yoipa kwambiri yotsutsana ndi Mariya,