153

Q.S An-Nisa (4:153)

يَسْـَٔلُكَ اَهْلُ الْكِتٰبِ اَنْ تُنَزِّلَ عَلَيْهِمْ كِتٰبًا مِّنَ السَّمَاۤءِ فَقَدْ سَاَلُوْا مُوْسٰٓى اَكْبَرَ مِنْ ذٰلِكَ فَقَالُوْٓا اَرِنَا اللّٰهَ جَهْرَةً فَاَخَذَتْهُمُ الصَّاعِقَةُ بِظُلْمِهِمْۚ ثُمَّ اتَّخَذُوا الْعِجْلَ مِنْۢ بَعْدِ مَا جَاۤءَتْهُمُ الْبَيِّنٰتُ فَعَفَوْنَا عَنْ ذٰلِكَ ۚ وَاٰتَيْنَا مُوْسٰى سُلْطٰنًا مُّبِيْنًا

yas'aluka ahlul-kitābi an tunazzila ‘alaihim kitābam minas-samā'i faqad sa'alū mūsā akbara min żālika fa qālū arinallāha jahratan fa akhażathumuṣ-ṣā‘iqatu bi ẓulmihim, ṡummattakhażul-‘ijla mim ba‘di mā jā'athumul-bayyinātu fa ‘afaunā ‘an żālik(a), wa ātainā mūsā sulṭānam mubīnā(n).

(Anthu a) Buku akukupempha (Muhammad) kuti uwatumizire buku kuchokera kumwamba. Ndithudi, iwo anapempha Mose chinthu chachikulu kuposa chimenecho. Iwo anati, “Tionetseni Mulungu m’choonadi.” Choncho anakanthidwa ndi mphezi chifukwa cha nkhanza zawo. Kenako analambira mwana wa ng’ombe, ataona zizindikiro zomveka bwino, koma tidawakhululukira, ndipo tidapatsa Mose mphamvu zenizeni.