150

Q.S An-Nisa (4:150)

اِنَّ الَّذِيْنَ يَكْفُرُوْنَ بِاللّٰهِ وَرُسُلِهٖ وَيُرِيْدُوْنَ اَنْ يُّفَرِّقُوْا بَيْنَ اللّٰهِ وَرُسُلِهٖ وَيَقُوْلُوْنَ نُؤْمِنُ بِبَعْضٍ وَّنَكْفُرُ بِبَعْضٍۙ وَّيُرِيْدُوْنَ اَنْ يَّتَّخِذُوْا بَيْنَ ذٰلِكَ سَبِيْلًاۙ

innal-lażīna yakfurūna billāhi wa rusulihī wa yurīdūna ay yufarriqū bainallāhi wa rusulihī wa yaqūlūna nu'minu biba‘ḍin wa nakfuru biba‘ḍ(in), wa yurīdūna ay yattakhiżū baina żālika sabīlā(n).

Ndithudi, amene sakhulupirira Mulungu ndi atumiki Ake, ndipo akufuna kusiyanitsa pakati pa (kukhulupirira) Mulungu ndi atumiki Ake, ponena kuti, "Timakhulupirira ena ndipo sitikhulupirira ena," ndipo akufuna kutenga njira yapakati (chikhulupiriro kapena kusakhulupirira),