14
Q.S An-Nisa (4:14)
وَمَنْ يَّعْصِ اللّٰهَ وَرَسُوْلَهٗ وَيَتَعَدَّ حُدُوْدَهٗ يُدْخِلْهُ نَارًا خَالِدًا فِيْهَاۖ وَلَهٗ عَذَابٌ مُّهِيْنٌ ࣖ
wa may ya‘ṣillāha wa rasūlahū wa yata‘adda ḥudūdahū yudkhilhu nāran khālidan fīhā, wa lahū ‘ażābum muhīn(un).
Ndipo aliyense amene samvera Allah ndi Mtumiki Wake ndi kuswa malire a lamulo Lake, Allah adzamuika ku moto wa Jahannamu, adzakhala komweko kwamuyaya ndipo adzalandira chilango chonyozetsa.