137
Q.S An-Nisa (4:137)
اِنَّ الَّذِيْنَ اٰمَنُوْا ثُمَّ كَفَرُوْا ثُمَّ اٰمَنُوْا ثُمَّ كَفَرُوْا ثُمَّ ازْدَادُوْا كُفْرًا لَّمْ يَكُنِ اللّٰهُ لِيَغْفِرَ لَهُمْ وَلَا لِيَهْدِيَهُمْ سَبِيْلًاۗ
innal-lażīna āmanū ṡumma kafarū ṡumma āmanū ṡumma kafarū ṡummazdādū kufral lam yakunillāhu liyagfira lahum wa lā liyahdiyahum sabīlā(n).
Ndithudi, amene akhulupirira kenako osakhulupirira, kenako n’kukhulupiriranso, kenako n’kukananso, kenako n’kuwonjezera kusakhulupirira kwawo, Mulungu sadzawakhululukira, kapena kuwasonyeza njira (yowongoka).