125

Q.S An-Nisa (4:125)

وَمَنْ اَحْسَنُ دِيْنًا مِّمَّنْ اَسْلَمَ وَجْهَهٗ لِلّٰهِ وَهُوَ مُحْسِنٌ وَّاتَّبَعَ مِلَّةَ اِبْرٰهِيْمَ حَنِيْفًا ۗوَاتَّخَذَ اللّٰهُ اِبْرٰهِيْمَ خَلِيْلًا

wa man aḥsanu dīnam mimman aslama wajhahū lillāhi wa huwa muḥsinuw wattaba‘a millata ibrāhīma ḥanīfā(n), wattakhażallāhu ibrāhīma khalīlā(n).

Ndipo ndani ali ndi chipembedzo chabwino kuposa munthu amene amadzipereka kwa Allah moona mtima, akuchita zabwino, ndikutsatira chipembedzo cholunjika cha Abrahamu? Ndipo Allah adasankha Abrahamu kukhala wokondedwa (Wake).