100

Q.S An-Nisa (4:100)

۞ وَمَنْ يُّهَاجِرْ فِيْ سَبِيْلِ اللّٰهِ يَجِدْ فِى الْاَرْضِ مُرٰغَمًا كَثِيْرًا وَّسَعَةً ۗوَمَنْ يَّخْرُجْ مِنْۢ بَيْتِهٖ مُهَاجِرًا اِلَى اللّٰهِ وَرَسُوْلِهٖ ثُمَّ يُدْرِكْهُ الْمَوْتُ فَقَدْ وَقَعَ اَجْرُهٗ عَلَى اللّٰهِ ۗوَكَانَ اللّٰهُ غَفُوْرًا رَّحِيْمًا ࣖ

wa may yuhājir fī sabīlillāhi yajid fil-arḍi murāgaman kaṡīraw wa sa‘ah(tan), wa may yakhruj mim baitihī muhājiran ilallāhi wa rasūlihī ṡumma yudrik-hul-mautu faqad waqa‘a ajruhū ‘alallāh(i), wa kānallāhu gafūrar raḥīmā(n).

Ndipo aliyense amene asamuka m’njira ya Allah, adzapeza padziko lapansi malo otakata osamuka ndi zinthu zambiri (zakudya). Aliyense amene watuluka m’nyumba mwake ndi cholinga chosamuka chifukwa cha Allah ndi Mtumiki Wake, kenako imfa imamugwera (asanafike komwe akupita), ndiye kuti mphotho yake yakhazikika kwa Allah. Ndipo Allah ndi Wokhululuka, Wachifundo Chambiri.