Q.S An-Nisa (4:1)
يٰٓاَيُّهَا النَّاسُ اتَّقُوْا رَبَّكُمُ الَّذِيْ خَلَقَكُمْ مِّنْ نَّفْسٍ وَّاحِدَةٍ وَّخَلَقَ مِنْهَا زَوْجَهَا وَبَثَّ مِنْهُمَا رِجَالًا كَثِيْرًا وَّنِسَاۤءً ۚ وَاتَّقُوا اللّٰهَ الَّذِيْ تَسَاۤءَلُوْنَ بِهٖ وَالْاَرْحَامَ ۗ اِنَّ اللّٰهَ كَانَ عَلَيْكُمْ رَقِيْبًا
yā ayyuhan-nāsuttaqū rabbakumul-lażī khalaqakum min nafsiw wāḥidatiw wa khalaqa minhā zaujahā wa baṡṡa minhumā rijālan kaṡīraw wa nisā'ā(n), wattaqullāhal-lażī tasā'alūna bihī wal-arḥām(a), innallāha kāna ‘alaikum raqībā(n).
Inu anthu! Opani Mbuye wanu amene anakulengani kuchokera mwa munthu mmodzi (Adamu), ndipo (Mulungu) analenga mnzake (Hava) kuchokera mwa iye mwini; ndipo kuchokera mwa onse awiriwa Mulungu analenga amuna ndi akazi ambiri. Opani Mulungu amene mumapemphana dzina lake, ndipo (sungani) ubale wa m'banja. Ndithudi, Mulungu nthawi zonse amakutetezani ndi kukusamalirani.