3
Q.S As-Sajdah (32:3)
اَمْ يَقُوْلُوْنَ افْتَرٰىهُ ۚ بَلْ هُوَ الْحَقُّ مِنْ رَّبِّكَ لِتُنْذِرَ قَوْمًا مَّآ اَتٰىهُمْ مِّنْ نَّذِيْرٍ مِّنْ قَبْلِكَ لَعَلَّهُمْ يَهْتَدُوْنَ
am yaqūlūnaftarāhu balhuwal-ḥaqqu mir rabbika litunżira qaumam mā atāhum min nażīrim min qablika la‘allahum yahtadūn(a).
Koma bwanji (osakhulupirira) akunena kuti, "Iye (Muhammad) ndiye wapeka." Ayi, Qur'an ndi choonadi (chomwe chinachokera) kwa Mbuye wako, kuti uchenjeze anthu omwe sanachezeredwepo ndi aliyense amene anakuchenjeza iwe usanakhalepo; kuti akapeze chitsogozo.