13

Q.S As-Sajdah (32:13)

وَلَوْ شِئْنَا لَاٰتَيْنَا كُلَّ نَفْسٍ هُدٰىهَا وَلٰكِنْ حَقَّ الْقَوْلُ مِنِّيْ لَاَمْلَـَٔنَّ جَهَنَّمَ مِنَ الْجِنَّةِ وَالنَّاسِ اَجْمَعِيْنَ

wa lau syi'nā la'ātainā kulla nafsin hudāhā wa lākin ḥaqqal-qaulu minnī la'amla'anna jahannama minal-jinnati wan-nāsi ajma‘īn(a).

Ndipo tikadafuna, tikadapatsa mzimu uliwonse chitsogozo (chake), koma mawu (lamulo) aperekedwa kuchokera kwa Ine akuti, "Ndidzadzaza Jahannama ndi ziwanda ndi anthu pamodzi."