83

Q.S Ali Imran (3:83)

اَفَغَيْرَ دِيْنِ اللّٰهِ يَبْغُوْنَ وَلَهٗ ٓ اَسْلَمَ مَنْ فِى السَّمٰوٰتِ وَالْاَرْضِ طَوْعًا وَّكَرْهًا وَّاِلَيْهِ يُرْجَعُوْنَ

afagaira dīnillāhi yabgūna wa lahū aslama man fis-samāwāti wal-arḍi ṭau‘aw wa ilaihi yurja‘ūn(a).

Nanga n’chifukwa chiyani akufunafuna zipembedzo zina kupatula chipembedzo cha Allah, pomwe chilichonse chakumwamba ndi chapadziko lapansi chimadzipereka kwa Iye, (kaya) mwakufuna kapena mopanda kufuna, ndipo kwa Iye yekha zimabwezedwa?