72
Q.S Ali Imran (3:72)
وَقَالَتْ طَّاۤىِٕفَةٌ مِّنْ اَهْلِ الْكِتٰبِ اٰمِنُوْا بِالَّذِيْٓ اُنْزِلَ عَلَى الَّذِيْنَ اٰمَنُوْا وَجْهَ النَّهَارِ وَاكْفُرُوْٓا اٰخِرَهٗ لَعَلَّهُمْ يَرْجِعُوْنَۚ
wa qālaṭ-ṭā'ifatum min ahlil-kitābi āminū bil-lażī unzila ‘alal-lażīna āmanū wajhan-nahāri wakfurū ākhirahū la‘allahum yarji‘ūn(a).
Ndipo gulu la anthu a m'buku linati (kwa wina ndi mnzake): "Khulupirirani zomwe zidavumbulutsidwa kwa okhulupirira kumayambiriro kwa tsiku ndipo zikane kumapeto, kuti abwerere (ku kusakhulupirira).