49

Q.S Ali Imran (3:49)

وَرَسُوْلًا اِلٰى بَنِيْٓ اِسْرَاۤءِيْلَ ەۙ اَنِّيْ قَدْ جِئْتُكُمْ بِاٰيَةٍ مِّنْ رَّبِّكُمْ ۙاَنِّيْٓ اَخْلُقُ لَكُمْ مِّنَ الطِّيْنِ كَهَيْـَٔةِ الطَّيْرِ فَاَنْفُخُ فِيْهِ فَيَكُوْنُ طَيْرًاۢ بِاِذْنِ اللّٰهِ ۚوَاُبْرِئُ الْاَكْمَهَ وَالْاَبْرَصَ وَاُحْيِ الْمَوْتٰى بِاِذْنِ اللّٰهِ ۚوَاُنَبِّئُكُمْ بِمَا تَأْكُلُوْنَ وَمَا تَدَّخِرُوْنَ ۙفِيْ بُيُوْتِكُمْ ۗاِنَّ فِيْ ذٰلِكَ لَاٰيَةً لَّكُمْ اِنْ كُنْتُمْ مُّؤْمِنِيْنَۚ

wa rasūlan ilā banī isrā'īl(a), annī qad ji'tukum bi'āyatim mir rabbikum, annī akhluqu lakum minaṭ-ṭīni kahai'atiṭ-ṭairi fa'anfukhu fihi fayakūnu ṭairam bi'iżnillāh(i), wa ubarri'ul-akmaha wal-abraṣa wa uḥyil-mautā bi'iżnillāh(i), wa unabbi'ukum bimā ta'kulūna wa mā taddakhirūna fī buyūtikum, inna fī żālika la'āyatal lakum in kuntum mu'minīn(a).

Ndipo monga Mtumwi kwa Ana a Israeli (adati), "Ndakudzerani ndi chizindikiro (chozizwitsa) chochokera kwa Mbuye wanu, ndiko kuti, ndidakupangirani (chinachake) kuchokera pansi chooneka ngati mbalame, kenako ndidachiuzira, ndipo chidasanduka mbalame ndi chilolezo cha Mulungu. Ndipo ndidachiritsa anthu omwe anali akhungu kuyambira kubadwa ndi anthu omwe anali ndi khate. Ndipo ndidapatsa moyo akufa ndi chilolezo cha Mulungu, ndipo ndikukuuzani zomwe mumadya ndi zomwe mumasunga m'nyumba mwanu. Ndithudi m'menemo muli chizindikiro (chowonadi cha utumidwa wanga) kwa inu, ngati muli okhulupirira."