Q.S Ali Imran (3:30)
يَوْمَ تَجِدُ كُلُّ نَفْسٍ مَّا عَمِلَتْ مِنْ خَيْرٍ مُّحْضَرًا ۛوَمَا عَمِلَتْ مِنْ سُوْۤءٍ ۛ تَوَدُّ لَوْ اَنَّ بَيْنَهَا وَبَيْنَهٗٓ اَمَدًاۢ بَعِيْدًا ۗوَيُحَذِّرُكُمُ اللّٰهُ نَفْسَهٗ ۗوَاللّٰهُ رَءُوْفٌۢ بِالْعِبَادِ ࣖ
yauma tajidu kullu nafsim mā ‘amilat min khairim muḥḍarā(n), wa mā ‘amilat min sū'(in), tawaddu lau anna bainahā wa bainahū amadam ba‘īdā(n), wa yuḥażżirukumullāhu nafsah(ū), wallāhu ra'ūfum bil-‘ibād(i).
(Kumbukirani) tsiku (lomwe) mzimu uliwonse udzalandira (malipiro) a ntchito zabwino zomwe udachita, (komanso malipiro) a zoipa zomwe udachita. Ankayembekezera kuti padzakhala mtunda wautali pakati pa iye ndi tsiku limenelo. Ndipo Allah akukuchenjezani za Iye mwini (chilango). Allah ndi Wachifundo Chambiri kwa akapolo Ake.