22

Q.S Ali Imran (3:22)

اُولٰۤىِٕكَ الَّذِيْنَ حَبِطَتْ اَعْمَالُهُمْ فِى الدُّنْيَا وَالْاٰخِرَةِ ۖ وَمَا لَهُمْ مِّنْ نّٰصِرِيْنَ

ulā'ikal-lażīna ḥabiṭat a‘māluhum fid-dun-yā wal-ākhirah(ti), wa mā lahum min nāṣirīn(a).

Awa ndi anthu omwe ntchito yawo padziko lapansi ndi yamtsogolo ndi yopanda pake, ndipo alibe wowathandiza.