200
Q.S Ali Imran (3:200)
يٰٓاَيُّهَا الَّذِيْنَ اٰمَنُوا اصْبِرُوْا وَصَابِرُوْا وَرَابِطُوْاۗ وَاتَّقُوا اللّٰهَ لَعَلَّكُمْ تُفْلِحُوْنَ ࣖ
yā ayyuhal-lażīna āmanuṣbirū wa ṣābirū wa rabiṭū, wattaqullāha la‘allakum tufliḥūn(a).
Inu amene mwakhulupirira! Khalani oleza mtima ndipo limbitsani chipiriro chanu ndipo khalani maso (m'malire a dziko lanu) ndipo opani Mulungu kuti mukhale ndi mwayi.