195

Q.S Ali Imran (3:195)

فَاسْتَجَابَ لَهُمْ رَبُّهُمْ اَنِّيْ لَآ اُضِيْعُ عَمَلَ عَامِلٍ مِّنْكُمْ مِّنْ ذَكَرٍ اَوْ اُنْثٰى ۚ بَعْضُكُمْ مِّنْۢ بَعْضٍ ۚ فَالَّذِيْنَ هَاجَرُوْا وَاُخْرِجُوْا مِنْ دِيَارِهِمْ وَاُوْذُوْا فِيْ سَبِيْلِيْ وَقٰتَلُوْا وَقُتِلُوْا لَاُكَفِّرَنَّ عَنْهُمْ سَيِّاٰتِهِمْ وَلَاُدْخِلَنَّهُمْ جَنّٰتٍ تَجْرِيْ مِنْ تَحْتِهَا الْاَنْهٰرُۚ ثَوَابًا مِّنْ عِنْدِ اللّٰهِ ۗ وَاللّٰهُ عِنْدَهٗ حُسْنُ الثَّوَابِ

fastajāba lahum rabbuhum annī lā uḍī‘u ‘amala ‘āmilim minkum min żakarin au unṡā, ba‘ḍukum mim ba‘ḍ(in), fal-lażīna hājarū wa ukhrijū min diyārihim wa ūżū fī sabīlī wa qātalū wa qutilū la'ukaffiranna ‘anhum sayyi'ātihim wa la udkhilannahum jannātin tajrī min taḥtihal-anhār(u), ṡawābam min ‘indillāh(i), wallāhu ‘indahū ḥusnuṡ-ṡawāb(i).

Choncho Mbuye wawo adawayankha pempho lawo (ponena kuti), "Ndithudi, sindiwononga ntchito ya aliyense mwa inu amene akuchita zabwino, kaya mwamuna kapena mkazi, chifukwa ena mwa inu ndi (ochokera) kwa ena. Choncho amene anasamuka, nachotsedwa m'nyumba zawo, navulazidwa panjira yanga, namenyana, naphedwa, ndithudi ndidzawachotsa zoipa zawo ndi kuwalowetsa m'minda momwe mitsinje ikuyenda pansi pake, ngati mphotho yochokera kwa Mulungu. Ndipo kwa Mulungu kuli mphotho yabwino."