184
Q.S Ali Imran (3:184)
فَاِنْ كَذَّبُوْكَ فَقَدْ كُذِّبَ رُسُلٌ مِّنْ قَبْلِكَ جَاۤءُوْ بِالْبَيِّنٰتِ وَالزُّبُرِ وَالْكِتٰبِ الْمُنِيْرِ
fa in każżabūka faqad kużżiba rusulum min qablika jā'ū bil-bayyināti waz-zuburi wal-kitābil-munīr(i).
Kotero ngati akunamizani (Muhammad), ndiye (dziwani kuti) atumwi omwe analipo kale inu munalibe nawonso ananamizidwa (nawonso), anabweretsa zozizwitsa zenizeni, Zubur ndi Buku lomwe limapereka kufotokozera kwangwiro.