181
Q.S Ali Imran (3:181)
لَقَدْ سَمِعَ اللّٰهُ قَوْلَ الَّذِيْنَ قَالُوْٓا اِنَّ اللّٰهَ فَقِيْرٌ وَّنَحْنُ اَغْنِيَاۤءُ ۘ سَنَكْتُبُ مَا قَالُوْا وَقَتْلَهُمُ الْاَنْۢبِيَاۤءَ بِغَيْرِ حَقٍّۙ وَّنَقُوْلُ ذُوْقُوْا عَذَابَ الْحَرِيْقِ
laqad sami‘allāhu qaulal-lażīna qālū innallāha faqīruw wa naḥnu agniyā'(u), sanaktubu mā qālū wa qatlahumul-ambiyā'a bigairi ḥaqq(in), wa naqūlu żūqū ‘ażābal-ḥarīq(i).
Ndithudi, Allah wamva mawu a anthu (Ayuda) omwe amati, "Ndithudi Mulungu ndi wosauka ndipo ife ndife olemera." Tidzalemba mawu awo ndi zochita zawo zopha aneneri popanda chifukwa (cholungama), ndipo tidzawauza (kwa iwo), "Lawani chilango choyaka!"