18
Q.S Ali Imran (3:18)
شَهِدَ اللّٰهُ اَنَّهٗ لَآ اِلٰهَ اِلَّا هُوَۙ وَالْمَلٰۤىِٕكَةُ وَاُولُوا الْعِلْمِ قَاۤىِٕمًاۢ بِالْقِسْطِۗ لَآ اِلٰهَ اِلَّا هُوَ الْعَزِيْزُ الْحَكِيْمُ
syahidallāhu annahū lā ilāha illā huw(a), wal-malā'ikatu wa ulul-‘ilmi qā'imam bil-qisṭ(i), lā ilāha illā huwal-‘azīzul-ḥakīm(u).
Allah akunena kuti palibe mulungu wina koma Iye; (momwemonso) angelo ndi anthu odziwa bwino ntchito zawo omwe amasunga chilungamo, palibe mulungu wina koma Iye, Wamphamvuyonse, Wanzeru zonse.