16
Q.S Ali Imran (3:16)
اَلَّذِيْنَ يَقُوْلُوْنَ رَبَّنَآ اِنَّنَآ اٰمَنَّا فَاغْفِرْ لَنَا ذُنُوْبَنَا وَقِنَا عَذَابَ النَّارِۚ
allażīna yaqūlūna rabbanā innanā āmannā fagfir lanā żunūbanā wa qinā ‘ażāban-nār(i).
(Ndiye) amene amapemphera kuti, “Mbuye wathu, ife tikhulupiriradi, choncho tikhululukireni machimo athu ndipo mutiteteze ku chilango cha moto.