155

Q.S Ali Imran (3:155)

اِنَّ الَّذِيْنَ تَوَلَّوْا مِنْكُمْ يَوْمَ الْتَقَى الْجَمْعٰنِۙ اِنَّمَا اسْتَزَلَّهُمُ الشَّيْطٰنُ بِبَعْضِ مَا كَسَبُوْا ۚ وَلَقَدْ عَفَا اللّٰهُ عَنْهُمْ ۗ اِنَّ اللّٰهَ غَفُوْرٌ حَلِيْمٌ ࣖ

innal-lażīna tawallau minkum yaumal-taqal-jam‘ān(i), innamastazallahumusy-syaiṭānu biba‘ḍi mā kasabū, wa laqad ‘afallāhu ‘anhum, innallāha gafūrun ḥalīm(un).

Ndithudi, amene anabwerera m’mbuyo pakati panu pamene panali nkhondo pakati pa magulu awiriwa, Satana anawagwetsa pansi chifukwa cha zolakwa zina (machimo) zomwe adachita (kale), koma Mulungu wawakhululukiradi. Ndithudi, Mulungu ndi Wokhululuka Kwambiri, Wachifundo Chambiri.