153
Q.S Ali Imran (3:153)
۞ اِذْ تُصْعِدُوْنَ وَلَا تَلْوٗنَ عَلٰٓى اَحَدٍ وَّالرَّسُوْلُ يَدْعُوْكُمْ فِيْٓ اُخْرٰىكُمْ فَاَثَابَكُمْ غَمًّا ۢبِغَمٍّ لِّكَيْلَا تَحْزَنُوْا عَلٰى مَا فَاتَكُمْ وَلَا مَآ اَصَابَكُمْ ۗ وَاللّٰهُ خَبِيْرٌ ۢبِمَا تَعْمَلُوْنَ
iż tuṣ‘idūna wa lā talwūna ‘alā aḥadiw war-rasūlu yad‘ūkum fī ukhrākum fa aṡābakum gammam bigammil likailā taḥzanū ‘alā mā fātakum wa lā mā aṣābakum, wallāhu khabīrum bimā taṣna‘ūn(a).
(Kumbukirani) pamene munathamanga osayang'ana aliyense, pomwe Mtumiki (Muhammad) yemwe anali m'gulu lanu (anzanu) anakuitanani (gulu lomwe linathawa), kenako Mulungu anakubweretserani chisoni pambuyo pa chisoni, kuti musadandaulenso chifukwa cha zomwe zakuthawani ndi zomwe zakugwerani. Ndipo Mulungu amadziwa zomwe mumachita.