151
Q.S Ali Imran (3:151)
سَنُلْقِيْ فِيْ قُلُوْبِ الَّذِيْنَ كَفَرُوا الرُّعْبَ بِمَٓا اَشْرَكُوْا بِاللّٰهِ مَا لَمْ يُنَزِّلْ بِهٖ سُلْطٰنًا ۚ وَمَأْوٰىهُمُ النَّارُ ۗ وَبِئْسَ مَثْوَى الظّٰلِمِيْنَ
sanulqī fī qulūbil-lażīna kafarur-ru‘ba bimā asyrakū billāhi mā lam yunazzil bihī sulṭānā(n), wa ma'wāhumun nār(u), wa bi'sa maṡwaẓ-ẓālimīn(a).
Tidzaika mantha m'mitima ya osakhulupirira, chifukwa chakuti amaphatikiza Mulungu ndi zinthu zomwe Mulungu sanavumbulutse. Ndipo malo awo obwerera ndi ku Jahannama. Ndipo (kumeneko) ndi malo oipa kwambiri okhala (kwa) ochita zoipa.