145
Q.S Ali Imran (3:145)
وَمَا كَانَ لِنَفْسٍ اَنْ تَمُوْتَ اِلَّا بِاِذْنِ اللّٰهِ كِتٰبًا مُّؤَجَّلًا ۗ وَمَنْ يُّرِدْ ثَوَابَ الدُّنْيَا نُؤْتِهٖ مِنْهَاۚ وَمَنْ يُّرِدْ ثَوَابَ الْاٰخِرَةِ نُؤْتِهٖ مِنْهَا ۗ وَسَنَجْزِى الشّٰكِرِيْنَ
wa mā kāna linafsin an tamūta illā bi'iżnillāhi kitābam mu'ajjalā(n), wa may yurid ṡawābad-dun-yā nu'tihī minhā, wa may yurid ṡawābal-ākhirati nu'tihī minhā, wa sanajzisy-syākirīn(a).
Ndipo chamoyo chilichonse sichidzafa pokhapokha ngati Mulungu walola, monga nthawi yoikidwiratu. Aliyense amene akufuna mphotho ya dziko lapansi, ndithudi tidzamupatsa mphothoyo (yapadziko lapansi), ndipo aliyense amene akufuna mphotho ya tsiku lomaliza, tidzamupatsanso mphothoyo (yapambuyo pa moyo), ndipo tidzawalipira oyamikira.