123

Q.S Ali Imran (3:123)

وَلَقَدْ نَصَرَكُمُ اللّٰهُ بِبَدْرٍ وَّاَنْتُمْ اَذِلَّةٌ ۚ فَاتَّقُوا اللّٰهَ لَعَلَّكُمْ تَشْكُرُوْنَ

wa laqad naṣarakumullāhu bibadriw wa antum ażillah(tun), fattaqullāha la‘allakum tasykurūn(a).

Ndipo ndithudi, Mulungu adakuthandizani pankhondo ya Badr, ngakhale kuti munali ofooka. Choncho, opani Mulungu kuti muyamike Iye.