Q.S Ali Imran (3:118)
يٰٓاَيُّهَا الَّذِيْنَ اٰمَنُوْا لَا تَتَّخِذُوْا بِطَانَةً مِّنْ دُوْنِكُمْ لَا يَأْلُوْنَكُمْ خَبَالًاۗ وَدُّوْا مَا عَنِتُّمْۚ قَدْ بَدَتِ الْبَغْضَاۤءُ مِنْ اَفْوَاهِهِمْۖ وَمَا تُخْفِيْ صُدُوْرُهُمْ اَكْبَرُ ۗ قَدْ بَيَّنَّا لَكُمُ الْاٰيٰتِ اِنْ كُنْتُمْ تَعْقِلُوْنَ
yā ayyuhal-lażīna āmanū lā tattakhiżū biṭānatam min dūnikum lā ya'lūnakum khabālā(n), waddū mā ‘anittum, qad badatil-bagḍā'u min afwāhihim, wa mā tukhfī ṣudūruhum akbar(u), qad bayyannā lakumul-āyāti in kuntum ta‘qilūn(a).
Inu amene mwakhulupirira! Musawachite mabwenzi anthu omwe sali m'gulu lanu (a chipembedzo chomwecho) omwe mumawadziwa, chifukwa nthawi zonse amakuvutitsani. Amafuna kuwonongani. Ndithudi, chidani chaonekera m'kamwa mwawo, ndipo zomwe mitima yawo imabisa ndizoipa kwambiri. Ndithudi, Takudziwitsani ma aya (Athu), ngati mumvetsetsa.