11

Q.S Ali Imran (3:11)

كَدَأْبِ اٰلِ فِرْعَوْنَۙ وَالَّذِيْنَ مِنْ قَبْلِهِمْۗ كَذَّبُوْا بِاٰيٰتِنَاۚ فَاَخَذَهُمُ اللّٰهُ بِذُنُوْبِهِمْ ۗ وَاللّٰهُ شَدِيْدُ الْعِقَابِ

kada'bi āli fir‘aun(a), wal-lażīna min qablihim, każżabū bi'āyātinā, fa'akhażahumullāhu biżunūbihim, wallāhu syadīdul-‘iqāb(i).

(Mkhalidwe wawo) unali ngati momwe zinalili kwa otsatira a Farao ndi omwe adalipo kale. Iwo adatsutsa mawu athu, kotero Mulungu adawalanga chifukwa cha machimo awo. Mulungu ndi woopsa kwambiri pa chilango.