101
Q.S Ali Imran (3:101)
وَكَيْفَ تَكْفُرُوْنَ وَاَنْتُمْ تُتْلٰى عَلَيْكُمْ اٰيٰتُ اللّٰهِ وَفِيْكُمْ رَسُوْلُهٗ ۗ وَمَنْ يَّعْتَصِمْ بِاللّٰهِ فَقَدْ هُدِيَ اِلٰى صِرَاطٍ مُّسْتَقِيْمٍ ࣖ
wa kaifa takfurūna wa antum tutlā ‘alaikum āyātullāhi wa fīkum rasūluh(ū), wa may ya‘taṣim billāhi faqad hudiya ilā ṣirāṭim mustaqīm(in).
Ndipo munakhala bwanji osakhulupirira pamene ma aya a Mulungu anawerengedwa kwa inu, ndipo Mtumiki Wake (Muhammad) anali pakati panu? Amene agwiritsitsa chipembedzo cha Mulungu, ndiye kuti adzatsogozedwa ku njira yolunjika.